December 28, 2020–January 3, 2021
LEVITIKO 16-17
Nyimbo Na. 41 ndi Pemphero
Mawu Oyamba (1 min.)
CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU
“Kodi Tsiku la Mwambo Wophimba Machimo Limakukhudzani Bwanji?”: (10 min.)
Le 16:12—Mkulu wa ansembe ankaonekera mophiphiritsira pamaso pa Yehova (w19.11 21 ¶4)
Le 16:13—Mkulu wa ansembe ankapereka zofukiza kwa Yehova (w19.11 21 ¶5)
Le 16:14, 15—Kenako mkulu wa ansembe ankapereka nsembe zophimba machimo a ansembe ndi anthu ena (w19.11 21 ¶6)
Kufufuza Mfundo Zothandiza: (10 min.)
Le 16:10—Kodi mbuzi ya Azazeli imaimira nsembe ya Yesu mu njira ziti? (it-1 226 ¶3)
Le 17:10, 11—N’chifukwa chiyani timakana kuikidwa magazi? (w14 11/15 10 ¶10)
Pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno, kodi mwapeza mfundo ziti zokhudza Yehova, utumiki kapena zinthu zina?
Kuwerenga Baibulo: (Osapitirira 4 min.) Le 16:1-17 (th phunziro 5)
KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI
Ulendo Woyamba: (Osapitirira 3 min.) Yambani ndi chitsanzo cha ulendo woyamba. Sonyezani mmene mungayankhire munthu amene wanena zinthu zina zomwe anthu amakonda kunena ngati sakufuna kuti tikambirane nawo. (th phunziro 3)
Ulendo Wobwereza: (Osapitirira 4 min.) Yambani ndi chitsanzo cha ulendo wobwereza. Kenako m’patseni chimodzi mwa zinthu zophunzitsira. (th phunziro 4)
Phunziro la Baibulo: (Osapitirira 5 min.) fg phunziro 1 ¶1-2 (th phunziro 14)
MOYO WATHU WACHIKHRISTU
“Kodi Mungakonde Kufunsira Sukulu ya Akhristu Olalikira za Ufumu?”: (15 min.) Nkhani yokambirana. Onerani vidiyo yakuti Amishonale Amagwira Ntchito Yokolola.
Phunziro la Baibulo la Mpingo: (Osapitirira 30 min.) jy mutu 114
Mawu Omaliza (Osapitirira 3 min.)
Nyimbo Na. 26 ndi Pemphero