December 7-13
LEVITIKO 10-11
Nyimbo Na. 32 ndi Pemphero
Mawu Oyamba (1 min.)
CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU
“Tizikonda Yehova Kuposa Mmene Timakondera Achibale Athu”: (10 min.)
Le 10:1, 2—Yehova anapha Nadabu ndi Abihu chifukwa chopereka moto wosaloledwa (it-1 1174)
Le 10:4, 5—Mitembo yawo inachotsedwa mumsasawo
Le 10:6, 7—Yehova analamula Aroni ndi ana ake ena kuti asasonyeze chisoni (w11 7/15 31 ¶16)
Kufufuza Mfundo Zothandiza: (10 min.)
Le 10:8-11—Kodi tikuphunzira chiyani pa mavesiwa? (w14 11/15 17 ¶18)
Le 11:8—Kodi Akhristu ayenera kupewa kudya nyama zoletsedwa m’Chilamulo cha Mose? (it-1 111 ¶5)
Pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno, kodi mwapeza mfundo ziti zokhudza Yehova, utumiki kapena zinthu zina?
Kuwerenga Baibulo: (Osapitirira 4 min.) Le 10:1-15 (th phunziro 10)
KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI
Vidiyo ya Ulendo Woyamba: (4 min.) Nkhani yokambirana. Onerani vidiyoyi. Kenako funsani mafunso awa: Kodi Tony anayankha bwanji zimene mwininyumba ananena pofuna kuti asakambirane ndi a Mboniwo? Kodi mungakambirane bwanji ndi munthu mfundo za pa Salimo 1:1, 2?
Ulendo Woyamba: (Osapitirira 4 min.) Yambani ndi chitsanzo cha ulendo woyamba. M’patseni kapepala komuitanira kumisonkhano yathu, kenako yerekezerani kumuonetsa vidiyo yakuti Kodi pa Nyumba ya Ufumu Pamachitika Zotani? (th phunziro 20)
Nkhani: (Osapitirira 5 min.) w11 2/15 12—Mutu: Kodi N’chiyani Chinakhazika Mtima Pansi Mose Atakwiyira Eleazara ndi Itamara? (th phunziro 12)
MOYO WATHU WACHIKHRISTU
“Timasonyeza Chikondi Tikamachita Zinthu Mogwirizana Ndi Chilango Chochokera kwa Yehova”: (15 min.) Nkhani yokambirana. Onerani vidiyo yakuti Pitirizani Kukhala Okhulupirika ndi Mtima Wonse.
Phunziro la Baibulo la Mpingo: (Osapitirira 30 min.) jy mutu 111 ndime 10-21
Mawu Omaliza (Osapitirira 3 min.)
Nyimbo Na. 150 ndi Pemphero