NDANDANDA YA UTUMIKI KOMANSO MOYO WATHU WACHIKHRISTU February 2016
Zitsanzo za Ulaliki
Zitsanzo za ulaliki wa Galamukani! ndi Mverani Mulungu. Gwiritsani ntchito zitsanzozi kuti mupange ulaliki wanu umene mungagwiritse ntchito.
CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU
Nehemiya Ankakonda Kulambira Yehova
Yerekezani kuti mukuona zimene Nehemiya anachita poyesetsa kuti amangenso mpanda n’kuthandiza anthu kuti azilambiranso Yehova. (Nehemiya 1-4)
CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU
Nehemiya Anali Woyang’anira Wabwino
Anathandiza Aisiraeli kuti azilambira Mulungu mosangalala. Yerekezani kuti mukuona zimene zinachitika ku Yerusalemu mwezi wa Tishri mu 455 B.C.E. (Nehemiya 8:1-18)
CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU
Anthu Okhulupirika Amatsatira Malangizo a Gulu la Yehova
Masiku a Nehemiya anthu anayambanso kulambira Yehova ndipo anachita zinthu zosiyanasiyana. (Nehemiya 9-11)
MOYO WATHU WACHIKHRISTU
Moyo Wabwino Kwambiri
Achinyamata akhoza kuchita zambiri m’gulu la Yehova. Gwiritsani ntchito mafunso awa pokambirana vidiyo.
CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU
Zimene Tikuphunzira kwa Nehemiya
Yerekezani kuti mukuona Nehemiya akuteteza mwakhama kulambira koona (Nehemiya 12-13)
MOYO WATHU WACHIKHRISTU
Itanirani Anthu Onse M’gawo Lanu ku Chikumbutso!
Chitsanzo cha ulaliki pogawira kapepala koitanira ku Chikumbutso cha 2016. Ngati munthu wasonyeza chidwi chitani zomwe tasonyeza
CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU
Esitere Anapulumutsa Anthu a Mulungu
Yerekezani kuti mukumuona Esitere akuteteza anthu a Mulungu molimba mtima. (Esitere 1-5)