February 1-7
NEHEMIYA 1-4
Nyimbo Na. 126 ndi Pemphero
Mawu Oyamba (Osapitirira 3 min.)
CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU
“Nehemiya Ankakonda Kulambira Yehova”: (10 min.)
[Onetsani vidiyo yakuti Mfundo Zothandiza Kumvetsa Buku la Nehemiya.]
Neh. 1:11; 2:1-3—Nehemiya ankasangalala chifukwa cholambira Yehova (w06 2/1 9 ndime 7)
Neh. 4:14—Nehemiya anadalira Yehova pamene ankatsutsidwa (w06 2/1 10 ndime 3)
Kufufuza Mfundo Zothandiza: (8 min.)
Neh. 1:1; 2:1—Kodi tikudziwa bwanji kuti chaka cha 20 chotchulidwa pa Nehemiya 1:1 n’chofanana ndi chotchulidwa pa Nehemiya 2:1? (w06 2/1 8 ndime 5)
Neh. 4:17, 18—Kodi zinkatheka bwanji kumanga ndi dzanja limodzi? (w06 2/1 9 ndime 1)
Kodi ndaphunzira chiyani zokhudza Yehova pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?
Kodi ndi mfundo ziti zimene ndaphunzira mlungu uno zimene ndingazigwiritse ntchito mu utumiki?
Kuwerenga Baibulo: Neh. 3:1-14 (Osapitirira 4 min.)
KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI
Konzekerani Zitsanzo za Ulaliki za Mwezi Uno: (15 min.) Nkhani yokambirana. Onetsani kavidiyo kosonyeza zitsanzo za ulaliki kenako kambiranani mfundo zimene mwaphunzirapo. Fotokozani zimene wofalitsa wachita kuti adzapange ulendo wobwereza. Limbikitsani omvera kuti alembe ulaliki umene angakonde kugwiritsa ntchito.
MOYO WATHU WACHIKHRISTU
Nyimbo Na. 103
Konzani Zoti Mudzachite Upainiya Wothandiza M’mwezi wa March Kapena April: (15 min.) Nkhani yokambirana. Gwiritsani ntchito mfundo zimene zili m’nkhani yakuti, “Zimene Mungachite Kuti Mudzasangalale M’nyengo ya Chikumbutso.” (km 2/14 2) Limbikitsani omvera kuti ayambe kukonzekera. (Miy. 21:5) Kenako funsani ofalitsa awiri amene anachitapo upainiya wothandiza kuti afotokoze mavuto amene anapirira komanso zosangalatsa zimene anapeza?
Phunziro la Baibulo la Mpingo: cl mutu 25 ndime 9-16 (30 min.)
Mfundo Zimene Taphunzira Komanso za Mlungu Wamawa (3 min.)
Nyimbo Na. 135 ndi Pemphero