February 27–March 5
YESAYA 63-66
Nyimbo Na. 19 ndi Pemphero
Mawu Oyamba (Osapitirira 3 min.)
CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU
“Tidzasangalala Kwambiri ndi Kumwamba Kwatsopano Komanso Dziko Lapansi Latsopano”: (10 min.)
Yes. 65:17
—“Zinthu zakale sizidzakumbukiridwanso” (ip-2 382 ¶23) Yes. 65:18, 19
—Tidzasangalala kwambiri (ip-2 384 ¶25) Yes. 65:21-23
—Tizidzagwira ntchito zosangalatsa ndipo sitidzakhalanso ndi nkhawa (w12 9/15 9 ¶4-5)
Kufufuza Mfundo Zothandiza: (8 min.)
Yes. 63:5
—Kodi ukali wa Mulungu umamuchirikiza bwanji? (w07 1/15 11 ¶7) Yes. 64:8
—Kodi Yehova amagwiritsa ntchito bwanji udindo wake monga Wotiumba? (w13 6/15 25 ¶3-5) Kodi ndaphunzira zotani zokhudza Yehova pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?
Kodi ndi mfundo ziti zimene ndaphunzira pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno zimene ndingazigwiritse ntchito mu utumiki?
Kuwerenga Baibulo: (Osapitirira 4 min.) Yes. 63:1-10
KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI
Ulendo Woyamba: (Osapitirira 2 min.) Aef. 5:33
—Kuphunzitsa Choonadi. Ulendo Wobwereza: (Osapitirira 4 min.) 1 Tim. 5:8; Tito 2:4, 5
—Kuphunzitsa Choonadi. Nkhani: (Osapitirira 6 min.) Yes. 66:23; w06 11/1 30-31 ¶14-17
—Mutu: Misonkhano Ndi Yofunika Kwambiri pa Kulambira Kwathu.
MOYO WATHU WACHIKHRISTU
Nyimbo Na. 129
“Tizisangalala ndi Chiyembekezo Chathu” (Yes. 65:17, 18; Aroma 12:12): (15 min.) Nkhani yokambirana. Onetsani vidiyo yakuti Tizisangalala ndi Chiyembekezo Chathu.
Phunziro la Baibulo la Mpingo: (30 min.) ia mutu 18 ¶14-21 komanso Mfundo Zofunika Kuziganizira patsamba 161
Mfundo Zimene Taphunzira Komanso za Mlungu Wamawa (3 min.)
Nyimbo Na. 95 ndi Pemphero