Pitani ku nkhani yake # link, for screen reader ##

Pitani ku mitu ya nkhani

MOYO WATHU WACHIKHRISTU

Mfundo Zimene Tingaphunzire Kuchokera M’mafanizo Onena za Ufumu

Mfundo Zimene Tingaphunzire Kuchokera M’mafanizo Onena za Ufumu

Yesu ankagwiritsa ntchito mafanizo osavuta kumva pophunzitsa mfundo zozama zachoonadi. Komabe, ndi anthu odzichepetsa okha amene ankamvetsa komanso kugwiritsa ntchito mfundo zomwe ankaphunzira m’mafanizowa. (Mat. 13:10-15) Pa mafanizo onena za Ufumu otsatirawa, yankhani mafunso awa: Kodi ndikuphunzira chiyani m’fanizoli? Kodi zimene ndikuphunzirazi ndingazigwiritse ntchito bwanji pa moyo wanga?

UFUMU WAKUMWAMBA ULI NGATI . . .