Ku Switzerland, akuona zimene Yehova analenga

NDANDANDA YA UTUMIKI KOMANSO MOYO WATHU WACHIKHRISTU February 2019

Zimene Tinganene

Zitsanzo za ulaliki zosonyeza kuti Baibulo n’lothandiza masiku ano.

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

Pitirizani Kuphunzitsa Chikumbumtima Chanu

Chikumbumtima chathu chingatithandize kusankha bwino zochita tikamachiphunzitsa pogwiritsa ntchito mfundo za m’Baibulo.

MOYO WATHU WACHIKHRISTU

Kodi Mumaona Makhalidwe a Mulungu Osaoneka ndi Maso?

Zimene timaona m’chilengedwe, zimatithandiza kuzindikira kuti Mulungu ali ndi makhalidwe monga mphamvu, chikondi, nzeru, chilungamo komanso kuwolowa manja.

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

“Mulungu Akuonetsa Chikondi Chake Kwa Ife”

Kodi tingasonyeze bwanji kuti timayamikira mphatso ya dipo?

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

Kodi ‘Mukudikira Mwachidwi’?

Kodi mungasonyeze bwanji kuti ‘mukudikira mwachidwi nthawi imene ulemelero wa ana a Mulungu udzaonekere’?

MOYO WATHU WACHIKHRISTU

Pitirizani Kudikira Mopirira

Kodi n’chiyani chingatithandize kudikira mopirira tikakumana ndi mayesero?

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

Fanizo la Mtengo wa Maolivi

Kodi mbali zosiyanasiyana za fanizo la mtengo wa maolivi zimaimira chiyani?

MOYO WATHU WACHIKHRISTU

Kuwonjezera Luso Lathu mu Utumiki​—Kusiya Kuphunzira ndi Munthu Yemwe Sakupita Patsogolo

Kodi tingatani ngati munthu amene taphunzira naye Baibulo kwa nthawi yaitali ndithu sakupita patsogolo?