February 11-17
AROMA 4-6
Nyimbo Na. 20 ndi Pemphero
Mawu Oyamba (Osapitirira 3 min.)
CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU
“Mulungu Akuonetsa Chikondi Chake Kwa Ife”: (10 min.)
Aroma 5:8, 12—Yehova anatikonda ngakhale kuti ndife “ochimwa” (w11 6/15 12 ¶5)
Aroma 5:13, 14—Uchimo ndi imfa zakhala zikulamulira ngati mfumu (w11 6/15 12 ¶6)
Aroma 5:18, 21—Yehova anatumiza Mwana wake kuti tidzapeze moyo (w11 6/15 12-13 ¶9-10)
Kufufuza Mfundo Zothandiza: (8 min.)
Aroma 6:3-5—Kodi kubatizidwa “mu mgwirizano ndi Khristu Yesu” komanso “mu imfa yake” kumatanthauza chiyani? (w08 6/15 29 ¶7)
Aroma 6:7—N’chifukwa chiyani anthu amene adzaukitsidwe sadzaweruzidwa chifukwa cha machimo amene anachita asanamwalire? (w14 6/1 11 ¶1)
Kodi mwaphunzira zotani zokhudza Yehova pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?
Kodi ndi mfundo zina ziti zothandiza zimene mwapeza pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?
Kuwerenga Baibulo: (Osapitirira 4 min.) Aroma 4:1-15 (th phunziro 10)
KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI
Vidiyo ya Ulendo Woyamba: (4 min.) Onerani ndi kukambirana mfundo za m’vidiyoyi.
Ulendo Woyamba: (Osapitirira 2 min.) Gwiritsani ntchito chitsanzo cha ulendo woyamba. (th phunziro 4)
Ulendo Woyamba: (Osapitirira 3 min.) Yambani ndi chitsanzo cha ulendo woyamba. Sonyezani mmene mungayankhire pa nkhani inayake yomwe anthu a m’gawo lanu amatsutsa kawirikawiri. (th phunziro 6)
Ulendo Woyamba: (Osapitirira 3 min.) Yambani ndi chitsanzo cha ulendo woyamba. Kenako musonyezeni chimodzi mwa zinthu zimene timagwiritsa ntchito pophunzira ndi anthu. (th phunziro 9)
MOYO WATHU WACHIKHRISTU
Zofunika Pampingo: (15 min.)
Phunziro la Baibulo la Mpingo: (30 min.) jy mutu 25
Mfundo Zimene Taphunzira Komanso za Mlungu Wamawa (3 min.)
Nyimbo Na. 17 ndi Pemphero