February 18-24
AROMA 7-8
Nyimbo Na. 27 ndi Pemphero
Mawu Oyamba (Osapitirira 3 min.)
CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU
“Kodi ‘Mukudikira Mwachidwi’?”: (10 min.)
Aroma 8:19—“Ulemerero wa ana a Mulungu” uonekera posachedwapa (w12 7/15 11 ¶17)
Aroma 8:20—“Chilengedwe chinaperekedwa ku mkhalidwe wopanda pake . . . pa maziko a chiyembekezo” (w12 3/15 23 ¶11)
Aroma 8:21—Chilengedwe “chidzamasulidwa ku ukapolo wa kuvunda” (w12 3/15 23 ¶12)
Kufufuza Mfundo Zothandiza: (8 min.)
Aroma 8:6—Kodi “kuika maganizo pa zinthu za thupi,” kumasiyana bwanji ndi “kuika maganizo pa zinthu za mzimu”? (w17.06 3)
Aroma 8:26, 27—Kodi Yehova amayankha bwanji “madandaulo amene sitinathe kuwafotokoza”? (w09 11/15 7 ¶20)
Kodi mwaphunzira zotani zokhudza Yehova pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?
Kodi ndi mfundo zina ziti zothandiza zimene mwapeza pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?
Kuwerenga Baibulo: (Osapitirira 4 min.) Aroma 7:13-25 (th phunziro 10)
KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI
Vidiyo ya Ulendo Wobwereza Woyamba: (5 min.) Onerani ndi kukambirana mfundo za m’vidiyoyi.
Ulendo Wobwereza Woyamba: (Osapitirira 3 min.) Gwiritsani ntchito chitsanzo cha ulendo wobwereza woyamba. (th phunziro 6)
Ulendo Wobwereza Woyamba: (Osapitirira 5 min.) Yambani ndi chitsanzo cha ulendo wobwereza woyamba. Musonyezeni ndi kukambirana mfundo za m’vidiyo yakuti Kodi Phunziro la Baibulo Limachitika Bwanji? (koma musaonetse vidiyoyi). (th phunziro 9)
MOYO WATHU WACHIKHRISTU
“Pitirizani Kudikira Mopirira”: (15 min.) Nkhani yokambirana. Onerani vidiyo yakuti Tiyenera ‘Kuthamanga Mopirira’—Musamakayikire Kuti Mudzapeza Mphoto.
Phunziro la Baibulo la Mpingo: (30 min.) jy mutu 26
Mfundo Zimene Taphunzira Komanso za Mlungu Wamawa (3 min.)
Nyimbo Na. 105 ndi Pemphero