February 4-10
AROMA 1-3
Nyimbo Na. 88 ndi Pemphero
Mawu Oyamba (Osapitirira 3 min.)
CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU
“Pitirizani Kuphunzitsa Chikumbumtima Chanu”: (10 min.)
[Onetsani vidiyo yakuti Mfundo Zothandiza Kumvetsa Buku la Aroma.]
Aroma 2:14, 15—Aliyense ali ndi chikumbumtima (lv 16 ¶6)
Aroma 2:15—Tiyenera kuphunzitsa chikumbumtima chathu kuti chizitithandiza kusankha zinthu moyenera (lv 17-18 ¶8-9)
Kufufuza Mfundo Zothandiza: (8 min.)
Aroma 3:4—Kodi timalola kuti “Mulungu akhale wonena zoona” m’njira yotani? (w08 6/15 30 ¶5)
Aroma 3:24, 25—Kodi “dipo lolipiridwa ndi Khristu Yesu” limaphimba bwanji “machimo amene anachitika kale” dipolo lisanaperekedwe? (w08 6/15 29 ¶6)
Kodi mwaphunzira zotani zokhudza Yehova pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?
Kodi ndi mfundo zina ziti zothandiza zimene mwapeza pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?
Kuwerenga Baibulo: (Osapitirira 4 min.) Aroma 1:1-17 (th phunziro 10)
KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI
Kuwerenga Komanso Kuphunzitsa Mwaluso: (10 min.) Nkhani yokambirana. Onerani vidiyo yakuti Kulankhulana Mokambirana ndi Anthu, kenako kambiranani phunziro 2 m’kabuku ka Kuphunzitsa.
Nkhani: (Osapitirira 5 min) w06 6/1 12-13—Mutu: Tizikumbukira Kuti Pali Zinthu Zina Zimene Ifeyo Kapena Ena Sangathe Kuchita. (th phunziro 7)
MOYO WATHU WACHIKHRISTU
“Kodi Mumaona Makhalidwe a Mulungu Osaoneka ndi Maso?”: (15 min.) Nkhani yokambirana. Onetsani vidiyo yakuti Zachilengedwe Zimatiphunzitsa za Ulemerero wa Mulungu—Kuwala Komanso Mitundu ya Zinthu.
Phunziro la Baibulo la Mpingo: (30 min.) jy mutu 24
Mfundo Zimene Taphunzira Komanso za Mlungu Wamawa (3 min.)
Nyimbo Na. 58 ndi Pemphero