Pitani ku nkhani yake # link, for screen reader ##

Pitani ku mitu ya nkhani

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU | AROMA 1-3

Pitirizani Kuphunzitsa Chikumbumtima Chanu

Pitirizani Kuphunzitsa Chikumbumtima Chanu

2:14, 15

Chikumbumtima chathu chingatithandize kusankha bwino zochita ngati . . .

  1. timachiphunzitsa pogwiritsa ntchito mfundo za m’Baibulo

  2. timachimvera chikamatikumbutsa mfundozo

  3. timapempha mzimu woyera kuti utithandize kulimbana ndi matupi athu ochimwawa.​—Aroma 9:1