Pitani ku nkhani yake # link, for screen reader ##

Pitani ku mitu ya nkhani

January 2-8

YESAYA 24-28

January 2-8
  • Nyimbo Na. 12 ndi Pemphero

  • Mawu Oyamba (Osapitirira 3 min.)

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

  • Yehova Amasamalira Anthu Ake”: (10 min.)

  • Kufufuza Mfundo Zothandiza: (8 min.)

    • Yes. 26:15—Kodi tingathandize bwanji Yehova pamene ‘akufutukulira kutali malire onse a dzikoli’? (w15 7/15 11 ¶18)

    • Yes. 26:20—Kodi zikuoneka kuti ‘zipinda zamkati’ zikuimira chiyani? (w13 3/15 23 ¶15-16)

    • Kodi ndaphunzira zotani zokhudza Yehova pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?

    • Kodi ndi mfundo ziti zimene ndaphunzira pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno zimene ndingazigwiritse ntchito mu utumiki?

  • Kuwerenga Baibulo: (Osapitirira 4 min.) Yes. 28:1-13

KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI

  • Kukonzekera Ulaliki wa Mwezi Uno: (15 min.) Nkhani yokambirana. Pambuyo poonetsa vidiyo ya chitsanzo cha ulaliki iliyonse, kambiranani mfundo zikuluzikulu za m’vidiyoyo. Dziwani izi: Palibe vidiyo ya chitsanzo cha ulaliki wa kapepala kakuti Kodi Mukufuna Kudziwa Choonadi? Choncho pemphani ofalitsa awiri kuti achite chitsanzo cha mmene tingagawirire kapepalaka.

MOYO WATHU WACHIKHRISTU