Pitani ku nkhani yake # link, for screen reader ##

Pitani ku mitu ya nkhani

January 29–February 4

Mateyu 10-11

January 29–February 4
  • Nyimbo Na. 4 ndi Pemphero

  • Mawu Oyamba (Osapitirira 3 min.)

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

  • Yesu Ankatsitsimula Ena”: (10 min.)

    • Mat. 10:29, 30​—Zimene Yesu ananena zoti Yehova amawerengera aliyense wa ife ndi zolimbikitsa (“Mpheta amazigulitsa kakhobidi kamodzi kochepa mphamvu” “tsitsi lenilenilo la m’mutu mwanu amaliwerenga” mfundo zimene ndikuphunzira, pa Mat. 10:29, nwtsty)

    • Mat. 11:28​—Kutumikira Yehova ndi kotsitsimula kwambiri (“olemedwa” “ndidzakutsitsimutsani” mfundo zimene ndikuphunzira pa Mat. 11:28, nwtsty)

    • Mat. 11:29, 30​—Kugonjera ulamuliro wa Khristu komanso kumvera malangizo ake kumatitsitsimula (“senzani goli” langa mfundo zimene ndikuphunzira pa Mat. 11:29, nwtsty)

  • Kufufuza Mfundo Zothandiza: (8 min.)

    • Mat. 11:2, 3​—Kodi n’chifukwa chiyani Yohane M’batizi anafunsa funso limeneli? (jy 96 ¶2-3)

    • Mat. 11:16-19​—Kodi mavesi amenewa akutanthauza chiyani? (jy 98 ¶1-2)

    • Kodi mwaphunzira zotani zokhudza Yehova pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?

    • Kodi ndi mfundo zina ziti zothandiza zimene mwapeza pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?

  • Kuwerenga Baibulo: (Osapitirira 4 min.) Mat. 11:1-19

KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI

  • Ulendo Wobwereza Wachiwiri: (Osapitirira 3 min.) Onani chitsanzo cha ulaliki.

  • Ulendo Wobwereza Wachitatu: (Osapitirira 3 min.) Sankhani lemba komanso funso loti mudzakambirane ulendo wotsatira.

  • Phunziro la Baibulo: (Osapitirira 6 min.) bhs 45-46 ¶15-16​—Muitanireni kumisonkhano yathu.

MOYO WATHU WACHIKHRISTU

  • Nyimbo Na. 87

  • Kutsitsimula Onse “Ogwira Ntchito Yolemetsa ndi Olemedwa”: (15 min.) Onetsani vidiyoyi Kenako kambiranani mafunso otsatirawa:

    • Kodi ndi zinthu ziti zimene zinachitika zomwe zinachititsa kuti anthu ena afunike kulimbikitsidwa?

    • Kodi Yehova ndi Yesu amalimbikitsa bwanji anthu kudzera m’gulu lathu?

    • Kodi Malemba amatilimbikitsa bwanji?

    • Kodi aliyense payekha angalimbikitse bwanji ena?

  • Phunziro la Baibulo la Mpingo: (30 min.) kr mutu 13 ¶24-32

  • Mfundo Zimene Taphunzira Komanso za Mlungu Wamawa (3 min.)

  • Nyimbo Na. 138 ndi Pemphero