January 8-14
MATEYU 4-5
Nyimbo Na. 82 ndi Pemphero
Mawu Oyamba (Osapitirira 3 min.)
CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU
“Zimene Tikuphunzira pa Zomwe Yesu Anaphunzitsa pa Ulaliki Wapaphiri”: (10 min.)
Mat. 5:3—Munthu amakhala wosangalala ngati amazindikira zosowa zake zauzimu (“Odala (osangalala kapena achimwemwe)” “anthu amene amazindikira zosowa zawo zauzimu” mfundo zimene ndikuphunzira pa Mat. 5:3, nwtsty)
Mat. 5:7—Munthu amakhala wosangalala akamasonyeza ena chifundo (“achifundo” mfundo zimene ndikuphunzira pa Mat. 5:7, nwtsty)
Mat. 5:9—Munthu amasangalala akamakhala mwamtendere ndi ena (“amene amabweretsa mtendere” mfundo zimene ndikuphunzira pa Mat. 5:9, nwtsty; w07 12/1 17)
Kufufuza Mfundo Zothandiza: (8 min.)
Mat. 4:9—Kodi Satana anayesa Yesu pomuuza kuti achite chiyani? (“kundiweramira kamodzi kokha” mfundo zimene ndikuphunzira pa Mat. 4:9, nwtsty)
Mat. 4:23—Kodi Yesu ankagwira ntchito ziwiri ziti zomwe ndi zofunika kwambiri? (“kuphunzitsa . . . kulalikira” mfundo zimene ndikuphunzira pa Mat. 4:23, nwtsty)
Kodi mwaphunzira zotani zokhudza Yehova pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?
Kodi ndi mfundo zina ziti zothandiza zimene mwapeza pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?
Kuwerenga Baibulo: (Osapitirira 4 min.) Mat. 5:31-48
KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI
Ulendo Woyamba: (Osapitirira 2 min.) Onani chitsanzo cha ulaliki.
Vidiyo ya Ulendo Wobwereza Woyamba: (5 min.) Onerani ndi kukambirana mfundo za m’vidiyoyi.
Nkhani: (Osapitirira 6 min.) w16.03 31-32—Mutu: Kodi Satana Anapitadi ndi Yesu Kukachisi Kapena Anangomuonetsa Masomphenya?
MOYO WATHU WACHIKHRISTU
Odala Ndi Anthu Amene Akuzunzidwa Chifukwa cha Chilungamo: (9 min.) Onetsani vidiyo yakuti Banja la a Namgung: Anamangidwa Chifukwa cha Chikhulupiriro Chawo, kenako kambiranani zimene tikuphunzira m’vidiyoyi.
“Kodi Tingatsatire Bwanji Malangizo Akuti Ukayanjane Ndi M’bale Wako Choyamba?”: (6 min.) Nkhani yokambirana. Kambiranani chifukwa chake mfundo yothera iliyonse m’mabokosi awiriwo ili yolondola.
Phunziro la Baibulo la Mpingo: (30 min.) kr mutu 12 ¶16-23, bokosi patsamba 125, 128 ndi 129
Mfundo Zimene Taphunzira Komanso za Mlungu Wamawa (3 min.)
Nyimbo Na. 141 ndi Pemphero