February 1-7
LEVITIKO 26-27
Nyimbo Na. 89 ndi Pemphero
Mawu Oyamba (1 min.)
CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU
“Kodi Mungatani Kuti Yehova Azikudalitsani?”: (10 min.)
Mfundo Zothandiza: (10 min.)
Le 26:16—Kodi tinganene kuti Yehova analanga bwanji Aisiraeli ndi matenda? (it-2 617)
Pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno, kodi mwapeza mfundo ziti zokhudza Yehova, utumiki kapena zinthu zina?
Kuwerenga Baibulo: (4 min.) Le 26:18-33 (th phunziro 10)
KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI
Ulendo Woyamba: (3 min.) Yambani ndi chitsanzo cha ulendo woyamba. Kenako musiyireni khadi lodziwitsa anthu za jw.org. (th phunziro 11)
Ulendo Wobwereza: (4 min.) Yambani ndi chitsanzo cha ulendo wobwereza. Kenako mugawireni chimodzi mwa Zinthu Zophunzitsira. (th phunziro 6)
Nkhani: (5 min.) w09 8/1 30—Mutu: Kodi Mulungu Amafuna Kuti Ndizipereka Ndalama Zingati? (th phunziro 16)
MOYO WATHU WACHIKHRISTU
“Sankhani Kutumikira Yehova”: (15 min.) Nkhani yokambirana. Onerani vidiyo yakuti Zimene Munthu Angachite Kuti Abatizidwe.
Phunziro la Baibulo la Mpingo: (30 min.) jy mutu 119
Mawu Omaliza (3 min.)
Nyimbo Na. 25 ndi Pemphero