Pitani ku nkhani yake # link, for screen reader ##

Pitani ku mitu ya nkhani

February 22-28

NUMERI 5–6

February 22-28

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI

MOYO WATHU WACHIKHRISTU

  • Nyimbo Na. 76

  • Kodi Mudzachita Upainiya Wothandiza M’mwezi wa March Kapena April?(5 min.) Nkhani yokambirana.

  • Ntchito Yoitanira Anthu ku Chikumbutso Idzayamba Loweruka pa 27 February: (10 min.) Nkhani yokambirana. Perekani kapepala koitanira anthu ku Chikumbutso kwa aliyense n’kukambirana mwachidule mfundo zake. Fotokozani zimene mpingo wanu wakonza kuti mudzakwanitse kuitanira anthu onse a m’gawo lanu. Onerani vidiyo ya zimene tinganene pogawira kapepalaka. Funsani omvera kuti: Kodi ndi nthawiiti pamene tiyenera kumuonetsa mwininyumba vidiyo yakuti, Tizikumbukira Imfa ya Yesu? Kodi mwininyumba angasonyeze chidwi m’njira ziti?

  • Phunziro la Baibulo la Mpingo: (30 min.) jy mutu 122

  • Mawu Omaliza (3 min.)

  • Nyimbo Na. 42 ndi Pemphero