February 8-14
NUMERI 1–2
Nyimbo Na. 123 ndi Pemphero
Mawu Oyamba (1 min.)
CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU
“Yehova Amachita Zinthu Mwadongosolo ndi Anthu Ake”: (10 min.)
Mfundo Zothandiza: (10 min.)
Nu 1:2, 3—N’chifukwa chiyani anthu ankalembedwa m’kaundula ku Isiraeli? (it-2 764)
Pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno, kodi mwapeza mfundo ziti zokhudza Yehova, utumiki kapena zinthu zina?
Kuwerenga Baibulo: (4 min.) Nu 1:1-19 (th phunziro 5)
KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI
Ulendo Woyamba: (3 min.) Yambani ndi chitsanzo cha ulendo woyamba. M’pempheni kuti muziphunzira naye Baibulo ndipo yerekezerani kumuonetsa vidiyo yakuti, Kodi Phunziro la Baibulo Limachitika Bwanji? (th phunziro 9)
Ulendo Wobwereza: (4 min.) Yambani ndi chitsanzo cha ulendo wobwereza. Sinthani ulaliki wanu kuti ugwirizane ndi nkhani imene mwininyumba watchula, ndipo werengani lemba logwirizana ndi nkhaniyo. (th phunziro 12)
Nkhani: (5 min.) w08 7/1 21—Mutu: N’chifukwa Chiyani Baibulo Limangotchula Mafuko 12 a Isiraeli Pomwe Kwenikweni Anali Mafuko 13? (th phunziro 7)
MOYO WATHU WACHIKHRISTU
“N’zotheka Kulalikira kwa Aliyense”: (10 min.) Nkhani yokambirana. Onerani vidiyo yakuti Khalani Bwenzi la Yehova—Muzilalikira Anthu Olankhula Chinenero cha Dziko Lina. Tchulani zina mwa zinthu zomwe zimapezeka mu pulogalamu ya JW Language®.
Zofunika Pampingo: (5 min.)
Phunziro la Baibulo la Mpingo: (30 min.) jy mutu 120
Mawu Omaliza (3 min.)
Nyimbo Na. 104 ndi Pemphero