January 25-31
LEVITIKO 24-25
Nyimbo Na. 144 ndi Pemphero
Mawu Oyamba (1 min.)
CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU
“Chaka cha Ufulu Komanso Ufulu Womwe Tidzakhale Nawo M’tsogolo”: (10 min.)
Mfundo Zothandiza: (10 min.)
Le 24:20—Kodi Mawu a Mulungu amaphunzitsa kuti munthu akatilakwira tizibwezera? (w09 9/1 22 ¶3)
Pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno, kodi mwapeza mfundo ziti zokhudza Yehova, utumiki kapena zinthu zina?
Kuwerenga Baibulo: (4 min.) Le 24:1-23 (th phunziro 10)
KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI
Ulendo Woyamba: (3 min.) Gwiritsani ntchito chitsanzo cha ulendo woyamba. Sonyezani mmene mungayankhire munthu amene wanena zinthu zina zomwe anthu amakonda kunena ngati sakufuna kuti tikambirane nawo. (th phunziro 16)
Ulendo Wobwereza: (4 min.) Yambani ndi chitsanzo cha ulendo wobwereza. M’patseni kapepala komuitanira kumisonkhano yathu ndipo yerekezerani kumuonetsa vidiyo yakuti, Kodi pa Nyumba ya Ufumu Pamachitika Zotani? kenako kambiranani naye mfundo za m’vidiyoyi. (th phunziro 11)
Phunziro la Baibulo: (5 min.) fg phunziro 12 ¶6-7 (th phunziro 14)
MOYO WATHU WACHIKHRISTU
Zofunika Pampingo (5 min.)
“Timathokoza Mulungu ndi Khristu Chifukwa cha Ufulu Womwe Tidzakhale Nawo”: (10 min.) Nkhani yokambirana. Onerani vidiyo yakuti, Pitirizani Kuyang’anitsitsa Yesu Pamene Mphepo Yamkuntho Ikubwera—Madalitso Amene Ufumu Udzabweretse.
Phunziro la Baibulo la Mpingo: (30 min.) jy mutu 118
Mawu Omaliza (3 min.)
Nyimbo Na. 109 ndi Pemphero