Pitani ku nkhani yake # link, for screen reader ##

Pitani ku mitu ya nkhani

Aisiraeli omwe anali akapolo akubwerera kwawo m’Chaka cha Ufulu

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

Chaka cha Ufulu Komanso Ufulu Womwe Tidzakhale Nawo M’tsogolo

Chaka cha Ufulu Komanso Ufulu Womwe Tidzakhale Nawo M’tsogolo

Chaka cha Ufulu chinkathandiza Aisiraeli kuti asamakhale ndi ngongole yosatha komanso asamakhale osauka mpaka kalekale (Le 25:10; it-1 871; onani chithunzi chapachikuto)

Malo ankagulitsidwa potengera kuchuluka kwa zokolola zomwe wogulayo adzapeze pamalowo (Le 25:15; it-1 1200 ¶2)

Yehova ankadalitsa anthu ake akamamvera lamulo lokhudza Chaka cha Ufulu (Le 25:​18-22; it-2 122-​123)

Posachedwapa, anthu okhulupirika adzasangalala ndi madalitso onse a Chaka cha Ufulu chophiphiritsa akadzamasulidwa ku uchimo ndi imfa.​—Aro 8:21.

Kodi tingatani kuti tidzapeze ufulu umene Yehova walonjeza?