January 4-10
LEVITIKO 18-19
Nyimbo Na. 122 ndi Pemphero
Mawu Oyamba (1 min.)
CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU
“Pitirizani Kukhala Ndi Makhalidwe Oyera”: (10 min.)
Mfundo Zothandiza: (10 min.)
Le 19:9, 10—Kodi Chilamulo chinkasonyeza bwanji kuti Mulungu amaganizira osauka? (w06 6/15 22 ¶11)
Pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno, kodi mwapeza mfundo ziti zokhudza Yehova, utumiki kapena zinthu zina?
Kuwerenga Baibulo: (4 min.) Le 18:1-15 (th phunziro 5)
KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI
Vidiyo ya Ulendo Woyamba: (5 min.) Nkhani yokambirana. Onerani vidiyo yakuti, Ulendo Woyamba: Pemphero—Sl 65:2. Muziimitsa nthawi iliyonse imene pali chizindikiro chosonyeza kuti muime n’kufunsa omvera mafunso omwe ali m’vidiyoyi.
Ulendo Woyamba: (3 min.) Gwiritsani ntchito chitsanzo cha ulendo woyamba. (th phunziro 3)
Nkhani: (5 min.) w02 2/1 29—Mutu: Kodi Malamulo Oletsa Ukwati Wapachibale Amene Ali M’Chilamulo cha Mose Amagwira Ntchito Bwanji kwa Akhristu Masiku Ano? (th phunziro 7)
MOYO WATHU WACHIKHRISTU
Khalani Bwenzi la Yehova—Tetezani Ana Anu: (5 min.) Nkhani yokambidwa ndi mkulu. Onerani vidiyoyi. Kenako fotokozani zimene tikuphunzirapo.—Miy 22:3.
“Makolo Muzithandiza Ana Anu Kukhala Odziwa Zinthu”: (10 min.) Nkhani yokambirana. Onerani vidiyo yakuti, Mangani Nyumba Yolimba—Muziteteza Ana Anu ku “Zinthu Zoipa.”
Phunziro la Baibulo la Mpingo: (30 min.) jy mutu 115
Mawu Omaliza (3 min.)
Nyimbo Na. 124 ndi Pemphero