January 18-24
LEVITIKO 22-23
Nyimbo Na. 86 ndi Pemphero
Mawu Oyamba (1 min.)
CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU
“Zikondwerero Zomwe Zimatikhudza”: (10 min.)
Mfundo Zothandiza: (10 min.)
Le 22:21, 22—N’chifukwa chiyani tiyenera kukhala okhulupirika kwa Yehova ndi mtima wathu wonse? (w19.02 3 ¶3)
Pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno, kodi mwapeza mfundo ziti zokhudza Yehova, utumiki kapena zinthu zina?
Kuwerenga Baibulo: (4 min.) Le 23:9-25 (th phunziro 5)
KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI
Ulendo Woyamba: (3 min.) Yambani ndi chitsanzo cha ulendo woyamba. Gawirani magazini yomwe ili ndi nkhani imene mwininyumba anatchula. (th phunziro 13)
Ulendo Wobwereza: (4 min.) Yambani ndi chitsanzo cha ulendo wobwereza. Kenako mugawireni chimodzi mwa Zinthu Zophunzitsira. (th phunziro 9)
Nkhani: (5 min.) w07 7/15 26—Mutu: Kodi Ndani Ankakolola Barele Woyamba Kucha N’kupita Naye Kukachisi? (th phunziro 13)
MOYO WATHU WACHIKHRISTU
“Misonkhano Yachigawo Imatipatsa Mwayi Wosonyezana Chikondi”: (15 min.) Nkhani yokambirana. Onerani vidiyo yakuti, Msonkhano Wamayiko Wakuti “Chikondi Sichitha.”
Phunziro la Baibulo la Mpingo: (30 min.) jy mutu 117
Mawu Omaliza (3 min.)
Nyimbo Na. 19 ndi Pemphero