February 21-27
1 SAMUELI 6-8
Nyimbo Na. 9 ndi Pemphero
Mawu Oyamba (1 min.)
CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU
“Kodi Mfumu Yanu ndi Ndani?”: (10 min.)
Mfundo Zothandiza: (10 min.)
1Sa 7:3—Kodi lembali likutiphunzitsa chiyani pa nkhani ya kutembenuka ndi kulapa? (w02 4/1 12 ¶13)
Pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno, kodi mwapeza mfundo ziti zokhudza Yehova, utumiki kapena zinthu zina?
Kuwerenga Baibulo: (4 min.) 1Sa 7:1-14 (th phunziro 2)
KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI
Ulendo Woyamba: (3 min.) Yambani ndi chitsanzo cha ulendo woyamba. Gawirani magazini yomwe ili ndi nkhani imene mwininyumba watchula. (th phunziro 12)
Ulendo Wobwereza: (4 min.) Yambani ndi chitsanzo cha ulendo wobwereza. Muitanireni kumisonkhano yathu. (th phunziro 18)
Phunziro la Baibulo: (5 min.) lffi phunziro 03 zomwe taphunzira, kubwereza komanso zolinga (th phunziro 20)
MOYO WATHU WACHIKHRISTU
Zofunika Pampingo: (10 min.)
Kodi Mudzachita Upainiya Wothandiza M’mwezi wa March Kapena April?: (5 min.) Nkhani yokambirana, yochokera mu nkhani yomwe ili mu Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu ka January-February 2021, tsamba 16.
Phunziro la Baibulo la Mpingo: (30 min.) lvs mutu 12 ndime 9-14, mawu akumapeto 27
Mawu Omaliza (3 min.)
Nyimbo Na. 29 ndi Pemphero