February 28–March 6
1 SAMUELI 9-11
Nyimbo Na. 121 ndi Pemphero
Mawu Oyamba (1 min.)
CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU
“Sauli Anali Wodzichepetsa Poyamba”: (10 min.)
Mfundo Zothandiza: (10 min.)
1Sa 9:9—Kodi n’kutheka kuti mawu a palembali ankatanthauza chiyani? (w05 3/15 22 ¶8)
Pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno, kodi mwapeza mfundo ziti zokhudza Yehova, utumiki kapena zinthu zina?
Kuwerenga Baibulo: (4 min.) 1Sa 9:1-10 (th phunziro 5)
KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI
““Zimene Mungachite Kuti Muzisangalala Kwambiri mu Utumiki—Muzithandiza Ophunzira Baibulo Kuti Asamacheze ndi Anthu Olakwika”: (10 min.) Nkhani yokambirana. Onerani vidiyo yakuti Muzithandiza Amene Mukuphunzira Nawo Baibulo Kuti Asamacheze ndi Anthu Olakwika.
Nkhani: (5 min.) w15 4/15 6-7 ¶16-20—Mutu: Mfundo Zomwe Zingathandize Pophunzitsa Ena. (th phunziro 19)
MOYO WATHU WACHIKHRISTU
Lipoti la Chaka Chautumiki: (15 min.) Nkhani yokambidwa ndi mkulu. Pambuyo powerenga chilengezo chochokera ku ofesi ya nthambi chokhudza lipoti la chaka chautumiki, funsani ofalitsa omwe munawasankhiratu kuti afotokoze zinthu zolimbikitsa zimene anakumana nazo mu utumiki chaka chathachi.
Phunziro la Baibulo la Mpingo: (30 min.) lvs mutu 12 ndime 15-22, mfundo za m’Baibulo tsa. 169-171
Mawu Omaliza (3 min.)
Nyimbo Na. 90 ndi Pemphero