Pitani ku nkhani yake # link, for screen reader ##

Pitani ku mitu ya nkhani

January 10-16

OWERUZA 17-19

January 10-16

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

  • Kusamvera Malamulo a Mulungu Kumabweretsa Mavuto”: (10 min.)

  • Mfundo Zothandiza: (10 min.)

    • Owe 19:18​—N’chifukwa chiyani dzina lakuti Yehova linaikidwa pa lembali mu Baibulo la Dziko Latsopano la Chingelezi lokonzedwanso mu 2013? (w15 12/15 10 ¶6)

    • Pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno, kodi mwapeza mfundo ziti zokhudza Yehova, utumiki kapena zinthu zina?

  • Kuwerenga Baibulo: (4 min.) Owe 17:1-13 (th phunziro 2)

KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI

MOYO WATHU WACHIKHRISTU

  • Nyimbo Na. 89

  • Khalani Bwenzi la Yehova​—Muzimvera Makolo Anu: (10 min.) Nkhani yokambirana. Onerani vidiyoyi. Kenako ngati n’zotheka, funsani ana omwe munawasankhiratu mafunso awa: Kodi Kalebe anasonyeza bwanji kuti sanamvere mayi ake? Nanga anakonza bwanji zimene analakwitsa? N’chifukwa chiyani muyenera kumvera makolo anu?

  • Zofunika Pampingo: (5 min.)

  • Phunziro la Baibulo la Mpingo: (30 min.) lvs mutu 10 ndime 13-18, mawu akumapeto 25

  • Mawu Omaliza (3 min.)

  • Nyimbo Na. 131 ndi Pemphero