Pitani ku nkhani yake # link, for screen reader ##

Pitani ku mitu ya nkhani

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

Kupereka Mnzako kwa Mdani N’koipa Kwambiri

Kupereka Mnzako kwa Mdani N’koipa Kwambiri

Delila anayesedwa kuti apereke Samisoni chifukwa cha ndalama (Owe 16:4, 5; w12 4/15 8 ¶4)

Delila anakakamiza Samisoni kuti aulule chinsinsi chake (Owe 16:15-18; w05 1/15 27 ¶4)

Akhristu ayenera kusonyeza kuti ndi okhulupirika m’banja komanso mumpingo (1At 2:10; w12 4/15 11-12 ¶15-16)

Yehova amadalitsa anthu okhulupirika.​—Sl 18:25, 26.