CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU
Muzikhala ndi Makhalidwe Abwino
Rute ankachita zinthu moganizira ena (Ru 3:10; w12 10/1 22 ¶5)
Rute ankadziwika kuti anali “mkazi wabwino kwambiri” (Ru 3:11; w12 10/1 23 ¶1)
Yehova anaona makhalidwe abwino amene Rute anali nawo ndipo anamudalitsa (Ru 4:11-13; w12 10/1 24 ¶3)
Lembani makhalidwe abwino amene mungakonde kuti muzidziwika nawo.