February 20-26
1 MBIRI 17-19
Nyimbo Na. 110 ndi Pemphero
Mawu Oyamba (1 min.)
CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU
“Muzikhalabe Wosangalala Ngakhale Pamene Zinthu Sizikuyenda Bwino”: (10 min.)
Mfundo Zothandiza: (10 min.)
1Mb 17:16-18—Mofanana ndi Davide, kodi tingakhale otsimikiza mtima za chiyani? (w20.02 12, bokosi)
Pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno, kodi mwapeza mfundo ziti zokhudza Yehova, utumiki kapena zinthu zina?
Kuwerenga Baibulo: (4 min.) 1Mb 18:1-17 (th phunziro 2)
KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI
Ulendo Woyamba: (3 min.) Yambani ndi nkhani imene ili mu chitsanzo cha ulendo woyamba. Yerekezerani kumuonetsa vidiyo yakuti Kodi a Mboni za Yehova ndi Anthu Otani? kenako kambiranani naye mfundo za muvidiyoyi. (th phunziro 17)
Ulendo Wobwereza: (4 min.) Yambani ndi nkhani imene ili mu chitsanzo cha ulendo wobwereza. Mugawireni chimodzi mwa Zinthu Zophunzitsira. (th phunziro 3)
Phunziro la Baibulo: (5 min.) lff phunziro 09 mfundo 4 (th phunziro 9)
MOYO WATHU WACHIKHRISTU
Lipoti la Chaka Chautumiki: (15 min.) Nkhani yokambirana. Pambuyo powerenga chilengezo chochokera ku ofesi ya nthambi chokhudza lipoti la chaka chautumiki, funsani omvera kuti afotokoze zinthu zabwino zomwe zili mu Lipoti la Chaka cha Utumiki cha 2022 la Mboni za Yehova Padziko Lonse. Funsani ofalitsa omwe munawasankhiratu kuti afotokoze zinthu zolimbikitsa zimene anakumana nazo mu utumiki chaka chathachi.
Phunziro la Baibulo la Mpingo: (30 min.) lff phunziro 38 mfundo 1-4
Mawu Omaliza (3 min.)
Nyimbo Na. 141 ndi Pemphero