February 6-12
1 MBIRI 10-12
Nyimbo Na. 94 ndi Pemphero
Mawu Oyamba (1 min.)
CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU
“Muzikhala Wofunitsitsa Kuchita Zimene Mulungu Amafuna”: (10 min.)
Mfundo Zothandiza: (10 min.)
1Mb 12:33—Kodi amuna 50,000 a fuko la Zebuloni anapereka bwanji chitsanzo chabwino? (it-1 1058 ¶5-6)
Pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno, kodi mwapeza mfundo ziti zokhudza Yehova, utumiki kapena zinthu zina?
Kuwerenga Baibulo: (4 min.) 1Mb 11:26-47 (th phunziro 5)
KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI
Ulendo Woyamba: (3 min.) Yambani ndi nkhani imene ili mu chitsanzo cha ulendo woyamba. M’pempheni kuti muziphunzira naye Baibulo. (th phunziro 12)
Ulendo Wobwereza: (4 min.) Yambani ndi nkhani imene ili mu chitsanzo cha ulendo wobwereza. Yerekezerani kumuonetsa vidiyo yakuti Kodi Phunziro la Baibulo Limachitika Bwanji? kenako kambiranani naye mfundo za muvidiyoyi. (th phunziro 6)
Phunziro la Baibulo: (5 min.) lff phunziro 09 mawu oyamba komanso mfundo 1-3 (th phunziro 18)
MOYO WATHU WACHIKHRISTU
“Muzidziwa Mmene Yehova Amaganizira”: (10 min.) Nkhani yokambirana komanso vidiyo.
“Khalani ndi Zolinga pa Nyengo ya Chikumbutso”: (5 min.) Nkhani yokambirana.
Phunziro la Baibulo la Mpingo: (30 min.) lff phunziro 37 mfundo 1-5
Mawu Omaliza (3 min.)
Nyimbo Na. 91 ndi Pemphero