CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU
Muzikhala Wofunitsitsa Kuchita Zimene Mulungu Amafuna
Sauli anali wosamvera, ndipo Yehova anamukana (1Mb 10:13, 14)
Yehova anasankha Davide kuti akhale mfumu m’malo mwa Sauli (1Mb 11:3)
Mosiyana ndi Sauli, Davide analola kuti malamulo komanso mfundo za Yehova zizimutsogolera (1Mb 11:15-19; w12 11/15 6 ¶12-13)
Davide ankakonda kuchita zimene Mulungu ankafuna. (Sl 40:8) Ifenso tingakhale ofunitsitsa kuchita zinthu zoyenera tikamaphunzira kuona zinthu mmene Yehova amazionera.—Sl 25:4; w18.06 17 ¶5-6.