January 2-8
2 MAFUMU 22-23
Nyimbo Na. 28 ndi Pemphero
Mawu Oyamba (1 min.)
CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU
“N’chifukwa Chiyani Kudzichepetsa N’kwabwino?”: (10 min.)
Mfundo Zothandiza: (10 min.)
2Mf 23:24, 25—Kodi chitsanzo cha Yosiya chingalimbikitse bwanji anthu amene anakulira m’banja limene anthu ake ankachita zoipa? (w01 4/15 26 ¶3-4)
Pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno, kodi mwapeza mfundo ziti zokhudza Yehova, utumiki kapena zinthu zina?
Kuwerenga Baibulo: (4 min.) 2Mf 23:16-25 (th phunziro 2)
KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI
Vidiyo ya Ulendo Woyamba: (5 min.) Nkhani yokambirana. Onerani vidiyo ya Ulendo Woyamba: Pemphero—Sl 65:2. Muziimitsa vidiyoyi nthawi iliyonse imene pali chizindikiro chosonyeza kuti muime n’kufunsa omvera mafunso omwe ali muvidiyoyi.
Ulendo Woyamba: (3 min.) Gwiritsani ntchito nkhani imene ili mu chitsanzo cha ulendo woyamba. (th phunziro 1)
Ulendo Woyamba: (5 min.) Yambani ndi nkhani imene ili mu chitsanzo cha ulendo woyamba, kenako yambitsani phunziro la Baibulo pogwiritsa ntchito phunziro 01 la kabuku kakuti Mungakhale Ndi Moyo Mpaka Kalekale. (th phunziro 16)
MOYO WATHU WACHIKHRISTU
Kodi N’kudzichepetsa Kapena N’kudzikweza? (Yak 4:6): (15 min.) Nkhani yokambirana. Onerani vidiyoyi. Kenako funsani mafunso otsatirawa: Kodi kudzichepetsa n’kosiyana bwanji ndi kudzikweza? Kodi tingaphunzire chiyani pa chitsanzo cha Mose? N’chifukwa chiyani muli wofunitsitsa kukhala wodzichepetsa?
Phunziro la Baibulo la Mpingo: (30 min.) lff phunziro 33
Mawu Omaliza (3 min.)
Nyimbo Na. 23 ndi Pemphero