Pitani ku nkhani yake # link, for screen reader ##

Pitani ku mitu ya nkhani

February 5-11

SALIMO 1-4

February 5-11

Nyimbo Na. 150 ndi Pemphero | Mawu Oyamba (1 min.)

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

1. Khalani ku Mbali ya Ufumu wa Mulungu

(10 min.)

[Onerani VIDIYO ya Mfundo Zothandiza Kumvetsa Buku la Masalimo.]

Maboma a anthu adzipanga kukhala adani a Mulungu (Sl 2:2; w21.09 15 ¶8)

Yehova akupereka mwayi kwa anthu onse kuti asankhe kukhala ku mbali ya Ufumu wake (Sl 2:10-12)

DZIFUNSENI KUTI, ‘Kodi ndine wotsimikiza mtima kusatenga nawo mbali pa zochitika za ndale za m’dzikoli, ngakhale zitaoneka kuti kuchita zimenezi kukhoza kundibweretsera mavuto?’—w16.04 29 ¶11.

2. Mfundo Zothandiza

(10 min.)

  • Sl 1:4—Kodi anthu oipa amafanana bwanji ndi “mankhusu amene amauluzika ndi mphepo”? (it-1 425)

  • Kodi ndi mfundo ziti zimene mwapeza pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?

3. Kuwerenga Baibulo

KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI

4. Kukambirana Mwachibadwa—Zomwe Filipo Anachita

(7 min.) Nkhani yokambirana. Onerani VIDIYO, kenako kambiranani lmd phunziro 2 mfundo 1-2.

5. Kukambirana Mwachibadwa—Zomwe Mungachite Potsanzira Filipo

(8 min.) Nkhani yokambirana kuchokera mu kabuku ka lmd phunziro 2 mfundo 3-5 ndi “Onaninso Malemba Awa.”

MOYO WATHU WA CHIKHRISTU

Nyimbo Na. 32

6. Zofunika Pampingo

(15 min.)

7. Phunziro la Baibulo la Mpingo

Mawu Omaliza (3 min.) | Nyimbo Na. 61 ndi Pemphero