January 1-7
YOBU 32-33
Nyimbo Na. 102 ndi Pemphero | Mawu Oyamba (1 min.)
1. Muzilimbikitsa Amene Akulimbana ndi Nkhawa
(10 min.)
Mukamachita zinthu ndi ena muziwaona kuti ndi anzanu (Yob 33:1; it-1 710)
Muzikhala achifundo ndipo musamawaweruze (Yob 33:6, 7; w14 6/15 25 ¶8-10)
Musanalankhule, muzimvetsera n’kuganizira ngati mmene anachitira Elihu (Yob 33:8-12, 17; w20.03 23 ¶17-18; Onani chithunzi chapachikuto)
2. Mfundo Zothandiza
(10 min.)
Yob 33:25—Kodi lembali likutithandiza bwanji kuti pamene tikukalamba tisamadere nkhawa za mmene tikuonekera? (w13 1/15 19 ¶10)
Kodi ndi mfundo ziti zimene mwapeza pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?
3. Kuwerenga Baibulo
(4 min.) Yob 32:1-22 (th phunziro 12)
4. Kuchita Chidwi ndi Anthu—Zomwe Yesu Anachita
(7 min.) Nkhani yokambirana. Onerani VIDIYO, kenako kambiranani kabuku ka lmd phunziro 1 mfundo 1-2.
5. Kuchita Chidwi ndi Anthu—Zomwe Mungachite Potsanzira Yesu
(8 min.) Nkhani yokambirana kuchokera mu kabuku ka lmd phunziro 1 mfundo 3-5 ndi “Onaninso Malemba Awa.”
Nyimbo Na. 116
6. Zofunika Pampingo
(15 min.)
7. Phunziro la Baibulo la Mpingo
(30 min.) bt mutu 4 bokosi patsamba 30
Mawu Omaliza (3 min.) |