Pitani ku nkhani yake # link, for screen reader ##

Pitani ku mitu ya nkhani

February 10-16

MASALIMO 147-150

February 10-16

Nyimbo Na. 12 ndi Pemphero | Mawu Oyamba (1 min.)

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

1. Tili Ndi Zifukwa Zambiri Zotamandira Ya

(10 min.)

Iye amasamalira aliyense payekha (Sl 147:3, 4; w17.07 18 ¶5-6)

Iye ndi wachifundo ndipo amagwiritsa ntchito mphamvu zake kuti atithandize (Sl 147:5; w17.07 18 ¶7)

Iye anatipatsa mwayi wokhala m’gulu la anthu ake (Sl 147:19, 20; w17.07 21 ¶18)


DZIFUNSENI KUTI, ‘Kodi n’chiyaninso chimandilimbikitsa kuti ndizitamanda Yehova?’

2. Mfundo Zothandiza

(10 min.)

  • Sl 148:1, 10—Kodi mbalame zimatamanda bwanji Yehova? (it-1 316)

  • Kodi ndi mfundo ziti zimene mwapeza pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?

3. Kuwerenga Baibulo

KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI

4. Ulendo Woyamba

(3 min.) KUNYUMBA NDI NYUMBA. Mwininyumba wakuuzani kuti akudwala matenda okhalitsa. (lmd phunziro 2 mfundo 5)

5. Ulendo Woyamba

(4 min.) KULALIKIRA MWAMWAYI. Pezani mwayi woti mumuuze zomwe mwaphunzira kumisonkhano yaposachedwapa. (lmd phunziro 4 mfundo 3)

6. Nkhani

(5 min.) w19.03 10 ¶7-11—Mutu: Muzimvera Yesu—Muzilalikira Uthenga Wabwino. Onani chithunzi. (th phunziro 14)

MOYO WATHU WA CHIKHRISTU

Nyimbo Na. 159

7. Lipoti la Chaka cha Utumiki

(15 min.) Nkhani yokambirana.

Pambuyo powerenga chilengezo chochokera ku ofesi ya nthambi chokhudza lipoti la chaka cha utumiki, funsani omvera kuti afotokoze zinthu zabwino zomwe zili mu Lipoti la Chaka cha Utumiki cha 2024 la Mboni za Yehova Padziko Lonse. Funsani ofalitsa omwe munawasankhiratu kuti afotokoze zinthu zolimbikitsa zimene anakumana nazo mu utumiki chaka chathachi.

8. Phunziro la Baibulo la Mpingo

Mawu Omaliza (3 min.) | Nyimbo Na. 37 ndi Pemphero