Pitani ku nkhani yake # link, for screen reader ##

Pitani ku mitu ya nkhani

February 17-23

MIYAMBO 1

February 17-23

Nyimbo Na. 88 ndi Pemphero | Mawu Oyamba (1 min.)

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

Mwana wa Solomo akumvetsera malangizo achikondi a bambo ake

1. Achinyamata, Kodi Mudzamvera Ndani?

(10 min.)

[Onerani VIDIYO yakuti Mfundo Zothandiza Kumvetsa Buku la Miyambo.]

Mukhale anzeru ndipo muzimvera makolo anu (Miy 1:8; w17.11 29 ¶16-17; onani chithunzi)

Musamamvere zonena za anthu amene amachita zoipa (Miy 1:10, 15; w05 2/15 19-20 ¶11-12)

2. Mfundo Zothandiza

(10 min.)

  • Miy 1:22—Kodi mawu akuti “wopusa” akagwiritsidwa ntchito m’Baibulo, amakhala akunena za ndani? (it-1 846)

  • Kodi ndi mfundo ziti zimene mwapeza pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?

3. Kuwerenga Baibulo

KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI

4. Ulendo Woyamba

(2 min.) KULALIKIRA M’MALO OPEZEKA ANTHU AMBIRI. Munthuyo akufuna kukangana nanu. (lmd phunziro 6 mfundo 5)

5. Ulendo Woyamba

(2 min.) KULALIKIRA M’MALO OPEZEKA ANTHU AMBIRI. Uzanani kumene mumakhala komanso patsanani manambala a foni ndi munthu amene wasonyeza chidwi (lmd phunziro 1 mfundo 5)

6. Ulendo Wobwereza

(2 min.) KULALIKIRA MWAMWAYI. Muuzeni kuti timaphunzira Baibulo ndi anthu ndipo m’patseni khadi lodziwitsa anthu za phunziroli. (lmd phunziro 9 mfundo 5)

7. Kuphunzitsa Anthu

(5 min.) lff phunziro 16 mfundo 6. Gwiritsani ntchito nkhani imene ili pagawo lakuti “Onani Zinanso” kuti muthandize wophunzira amene amakayikira ngati Yesu anachitadi zodabwitsa. (th phunziro 3)

MOYO WATHU WA CHIKHRISTU

Nyimbo Na. 89

8. Zofunika Pampingo

(15 min.)

9. Phunziro la Baibulo la Mpingo

(30 min.) bt mutu 22 ¶15-21

Mawu Omaliza (3 min.) | Nyimbo Na. 80 ndi Pemphero