January 13-19
MASALIMO 135-137
Nyimbo Na. 2 ndi Pemphero | Mawu Oyamba (1 min.)
1. “Ambuye Wathu Ndi Wamkulu Kuposa Milungu Ina Yonse”
(10 min.)
Yehova wasonyeza kuti iye ndi amene amatsogolera chilengedwe chonse (Sl 135:5, 6; it-2 661 ¶4-5)
Amateteza anthu ake (Eks 14:29-31; Sl 135:14)
Amakhala nafe tikafooka (Sl 136:23; w21.11 6 ¶16)
2. Mfundo Zothandiza
(10 min.)
3. Kuwerenga Baibulo
(4 min.) Sl 135:1-21 (th phunziro 11)
4. Ulendo Woyamba
(3 min.) KULALIKIRA MWAMWAYI. Uzanani kumene mumakhala komanso patsanani manambala a foni ndi munthu amene wasonyeza chidwi. (lmd phunziro 2 mfundo 4)
5. Ulendo Wobwereza
(4 min.) KUNYUMBA NDI NYUMBA. Muitanireni ku misonkhano yathu. (lmd phunziro 9 mfundo 4)
6. Kufotokoza Zimene Mumakhulupirira
(5 min.) Chitsanzo. ijwfq 7—Mutu: Kodi a Mboni za Yehova Ndi Akhristu? (th phunziro 12)
Nyimbo Na. 10
7. Zofunika Pampingo
(15 min.)
8. Phunziro la Baibulo la Mpingo
(30 min.) bt mutu 21 ¶1-7, bokosi patsamba 166