July 18-24
MASALIMO 74-78
Nyimbo Na. 110 ndi Pemphero
Mawu Oyamba (Osapitirira 3 min.)
CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU
“Tizikumbukira Ntchito za Yehova”: (10 min.)
Sal. 74:16; 77:6, 11, 12
—Tiziganizira ntchito za Yehova (w15 8/15 10 ndime 3-4; w04 3/1 19-20; w03 7/1 10 ndime 6-7) Sal. 75:4-7
—Ntchito ina imene Yehova amagwira ndi kusankha amuna oti azitsogolera mumpingo (w06 7/15 11 ndime 3; it-1-E 1160 ndime 7) Sal. 78:11-17
—Tizikumbukira mmene Yehova wakhala akupulumutsira atumiki ake (w04 4/1 21-22)
Kufufuza Mfundo Zothandiza: (8 min.)
Sal. 78:2
—Kodi lembali linakwaniritsidwa bwanji kudzera mwa Mesiya? (w11 8/15 11 ndime 14) Sal. 78:40, 41
—Mogwirizana ndi mavesi amenewa, kodi zochita zathu zingakhudze bwanji Yehova? (w12 11/1 14 ndime 5; w11 7/1 10) Kodi ndaphunzira chiyani zokhudza Yehova pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?
Kodi ndi mfundo ziti zimene ndaphunzira mlungu uno zimene ndingazigwiritse ntchito mu utumiki?
Kuwerenga Baibulo: (Osapitirira 4 min.) Sal. 78:1-21
KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI
Ulendo Woyamba: (Osapitirira 2 min.) wp16.4 tsamba 16
—Muuzeni kuti akhoza kupereka ndalama zothandizira ntchito yolalikira ngati akufuna. Ulendo Wobwereza: (Osapitirira 4 min.) wp16.4 tsamba 16
Phunziro la Baibulo: (Osapitirira 6 min.) fg phunziro 5 ndime 6 ndi 7
MOYO WATHU WACHIKHRISTU
Nyimbo Na. 15
Zofunika pampingo: (10 min.)
“Yehova . . . Analenga Zinthu Zonse”: (5 min.) Nkhani yokambirana. Onerani vidiyoyi yomwe imapezeka pa webusaiti ya jw.org/ny yakuti “Yehova . . . Analenga Zinthu Zonse.” (Pitani pamene palembedwa kuti ZIMENE BAIBULO LIMAPHUNZITSA > ANA.) Mukamaliza, itanani ana angapo kuti abwere kutsogolo ndipo afunseni mafunso okhudza vidiyoyi.
Phunziro la Baibulo la Mpingo: (30 min.) ia mutu 2 ndime 13-23
Mfundo Zimene Taphunzira Komanso za Mlungu Wamawa (3 min.)
Nyimbo Na. 73 ndi Pemphero