Msonkhano wapadera mumzinda wa Vienna ku Austria

NDANDANDA YA UTUMIKI KOMANSO MOYO WATHU WACHIKHRISTU July 2018

Zimene Tinganene

Zimene tinganene zokhudza mfundo za m’Baibulo zomwe zingathandize kuti mabanja azikhala osangalala.

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

Muzikhala Owolowa Manja

Munthu wowolowa manja amasangalala akamagwiritsa ntchito zinthu zake pothandiza komanso kulimbikitsa ena.

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

Kodi Chofunika N’chiyani Kuti Munthu Akhale Wotsatira wa Yesu?

Kodi tiyenera kumaganizira kwambiri chiyani ngati tayamba kusokonezedwa ndi zinthu zakumbuyo zimene tinasiya?

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

Fanizo la Msamariya Wachifundo

Otsatira a Yesu ayenera kuchita zonse zomwe angathe kuti azikonda ena, ngakhale omwe amasiyana nawo m’zinthu zambiri.

MOYO WATHU WACHIKHRISTU

N’chifukwa Chiyani Sitiyenera Kulowerera Ndale? (Mika 4:2)

Potsanzira Mulungu wathu yemwe ndi wopanda tsankho, tiyenera ‘kuchitira onse zabwino.’

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

“Ndinu Ofunika Kwambiri Kuposa Mpheta Zambiri”

Kodi tingatengere bwanji chitsanzo cha Yehova pa nkhani yoganizira anthu omwe akuzunzidwa?

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

Fanizo la Mwana Wolowerera

Kodi tikuphunzira chiyani mu fanizo la Yesu la mwana wolowerera pa nkhani ya nzeru, kudzichepetsa komanso kudalira Yehova?

MOYO WATHU WACHIKHRISTU

Mwana Wolowerera

Kodi tikuphunzira chiyani m’vidiyoyi?