Pitani ku nkhani yake # link, for screen reader ##

Pitani ku mitu ya nkhani

MOYO WATHU WACHIKHRISTU

N’chifukwa Chiyani Sitiyenera Kulowerera Ndale? (Mika 4:2)

N’chifukwa Chiyani Sitiyenera Kulowerera Ndale? (Mika 4:2)

Fanizo la Msamariya wachifundo limatithandiza kudziwa kuti Yehova ndi Mulungu wopanda tsankho. Iye amafuna kuti ‘tichitire onse zabwino’ kuphatikizapo anthu omwe timasiyana nawo maphunziro, mtundu, fuko kapena chipembedzo.​—Agal. 6:10; Mac. 10:34.

ONERANI VIDIYO YAKUTI, N’CHIFUKWA CHIYANI SITIYENERA KULOWERERA NDALE? (MIKA 4:2), KENAKO KAMBIRANANI MAFUNSO OTSATIRAWA:

  • Kodi timadziwa bwanji kuti lemba la Mika 4:2 limanena zimene zikuchitikira anthu a Mulungu masiku ano?

  • Kodi tingapewe bwanji ndale, nanga ubwino wake ndi wotani?

  • Kodi lemba la Chivumbulutso 13:16, 17, likusonyeza bwanji kuti andale amayesetsa kusokoneza maganizo komanso zochita zathu?

Kodi ndi zinthu zitatu ziti zomwe zingachititse kuti tiyambe kuchita nawo zandale kapena kukonda dziko lathu?