July 23-29
Luka 12-13
Nyimbo Na. 4 ndi Pemphero
Mawu Oyamba (Osapitirira 3 min.)
CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU
“Ndinu Ofunika Kwambiri Kuposa Mpheta Zambiri”: (10 min.)
Luka 12:6—Yehova samaiwala ngakhale mbalame zing’onozing’ono (“mpheta” mfundo zimene ndikuphunzira pa Luka 12:6, nwtsty)
Luka 12:7—Zimene Yehova amadziwa zokhudza anthufe, zimasonyeza kuti amatiganizira kwambiri (“ngakhale tsitsi lonse la m’mutu mwanu analiwerenga” mfundo zimene ndikuphunzira pa Luka 12:7, nwtsty)
Luka 12:7—Yehova amaona kuti munthu aliyense ndi wofunika (cl 241 ¶4-5)
Kufufuza Mfundo Zothandiza: (8 min.)
Luka 13:24—Kodi malangizo a Yesuwa akutanthauza chiyani? (“Yesetsani mwamphamvu” mfundo zimene ndikuphunzira pa Luka 13:24, nwtsty)
Luka 13:33—N’chifukwa chiyani Yesu ananena mawu amenewa? (“n’kosayenera” mfundo zimene ndikuphunzira pa Luka 13:33, nwtsty)
Kodi mwaphunzira zotani zokhudza Yehova pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?
Kodi ndi mfundo zina ziti zothandiza zimene mwapeza pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?
Kuwerenga Baibulo: (Osapitirira 4 min.) Luka 12:22-40
KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI
Ulendo Wobwereza Wachiwiri: (Osapitirira 3 min.) Yambani ndi chitsanzo cha zimene tinganene. Kenako muitanireni kumisonkhano yathu.
Ulendo Wobwereza Wachitatu: (Osapitirira 3 min.) Sankhani lemba lililonse ndipo gawirani buku kapena kabuku kamene timagwiritsa ntchito pophunzira ndi anthu.
Phunziro la Baibulo: (Osapitirira 6 min.) lv 185 ¶4-5
MOYO WATHU WACHIKHRISTU
Tisawaiwale Ngakhale Amakhala Kwaokha: (15 min.) Onerani vidiyoyi. Kenako kambiranani mafunso otsatirawa:
Kodi ndi mavuto otani omwe ofalitsa atatu a m’vidiyoyi anakumana nawo?
Kodi Yehova anasonyeza bwanji kuti sanawaiwale?
Kodi ofalitsawa amachita chiyani kuti apitirizebe kutumikira Yehova ngakhale akukumana ndi mavuto, nanga zimenezi zalimbikitsa bwanji ena?
Kodi tingasonyeze bwanji kuti timakonda achikulire komanso ena omwe akudwala mumpingo wathu?
Phunziro la Baibulo la Mpingo: (30 min.) kr mutu 22 ¶1-7
Mfundo Zimene Taphunzira Komanso za Mlungu Wamawa (3 min.)
Nyimbo Na. 5 ndi Pemphero