Pitani ku nkhani yake # link, for screen reader ##

Pitani ku mitu ya nkhani

July 9-15

Luka 8-9

July 9-15

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

  • Kodi Chofunika N’chiyani Kuti Munthu Akhale Wotsatira wa Yesu?”: (10 min.)

    • Luka 9:57, 58​—Anthu amene amatsatira Yesu ayenera kumakhulupirira kwambiri Yehova (it-2 494)

    • Luka 9:59, 60​—Anthu amene amatsatira Yesu amaika Ufumu wa Mulungu pamalo oyamba pamoyo wawo (“kukaika maliro a bambo anga” “Aleke akufa aike akufa awo” mfundo zimene ndikuphunzira pa Luka 9:59, 60, nwtsty)

    • Luka 9:61, 62​—Anthu amene amatsatira Yesu samalola kuti zinthu za m’dzikoli ziwasokoneze (“Kulima pogwiritsa ntchito pulawo” zithunzi ndi mavidiyo, nwtsty; w12 4/15 15-16 ¶11-13)

  • Kufufuza Mfundo Zothandiza: (8 min.)

    • Luka 8:3​—Kodi Akhristu amenewa ‘anatumikira’ bwanji Yesu komanso atumwi? (“anali kutumikira” mfundo zimene ndikuphunzira pa Luka 8:3, nwtsty)

    • Luka 9:49, 50​—N’chifukwa chiyani Yesu sanaletse munthu wina kutulutsa ziwanda ngakhale kuti sanali wotsatira wake? (w08 3/15 31 ¶3)

    • Kodi mwaphunzira zotani zokhudza Yehova pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?

    • Kodi ndi mfundo zina ziti zothandiza zimene mwapeza pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?

  • Kuwerenga Baibulo: (Osapitirira 4 min.) Luka 8:1-15

KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI

  • Ulendo Woyamba: (Osapitirira 2 min.) Gwiritsani ntchito chitsanzo cha zimene tinganene.

  • Vidiyo ya Ulendo Wobwereza Woyamba: (5 min.) Onerani ndi kukambirana mfundo za m’vidiyoyi.

  • Nkhani: (Osapitirira 6 min.) w12 3/15 27-28 ¶11-15​—Mutu: Kodi Tiyenera Kumanong’oneza Bondo Tikaganizira Zinthu Zimene Tinasiya Chifukwa cha Ufumu wa Mulungu?

MOYO WATHU WACHIKHRISTU