August 16-22
DEUTERONOMO 27-28
Nyimbo Na. 89 ndi Pemphero
Mawu Oyamba (1 min.)
CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU
“Madalitso Onsewa . . . Adzakupeza”: (10 min.)
Mfundo Zothandiza: (10 min.)
De 27:17—N’chifukwa chiyani Chilamulo cha Yehova chinkaletsa kusuntha chizindikiro cha malire a munthu wina? (it-1 360)
Pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno, kodi mwapeza mfundo ziti zokhudza Yehova, utumiki kapena zinthu zina?
Kuwerenga Baibulo: (4 min.) De 28:1-14 (th phunziro 11)
KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI
Ulendo Woyamba: (3 min.) Yambani ndi chitsanzo cha ulendo woyamba. Gawirani chimodzi mwa Zinthu Zophunzitsira. (th phunziro 6)
Ulendo Wobwereza: (4 min.) Yambani ndi chitsanzo cha ulendo wobwereza. M’patseni kapepala koitanira anthu kumisonkhano yathu ndipo kenako yerekezerani kumuonetsa vidiyo yakuti Kodi pa Nyumba ya Ufumu Pamachitika Zotani? (th phunziro 3)
Phunziro la Baibulo: (5 min.) lvs 234 ¶21-22 (th phunziro 9)
MOYO WATHU WACHIKHRISTU
“Mmene Chilengedwe Chimasonyezera Kuti Mulungu Ndi Wachikondi”: (15 min.) Nkhani yokambirana. Onerani vidiyo yakuti Chilengedwe Chimasonyeza Kuti Yehova Ndi Wachikondi.
Phunziro la Baibulo la Mpingo: (30 min.) lvs mutu 3 ndime 8-15
Mawu Omaliza (3 min.)
Nyimbo Na. 30 ndi Pemphero