August 2-8
DEUTERONOMO 22-23
Nyimbo Na. 1 ndi Pemphero
Mawu Oyamba (1 min.)
CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU
“Kodi Chilamulo Chinkasonyeza Bwanji Kuti Yehova Amaganizira Zinyama?”: (10 min.)
Mfundo Zothandiza: (10 min.)
De 23:19, 20—N’chifukwa chiyani mlendo akatenga ngongole ankafunika kupereka chiwongoladzanja pomwe Mwisiraeli sankafunika kupereka chiwongoladzanja? (it-1 600)
Pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno, kodi mwapeza mfundo ziti zokhudza Yehova, utumiki kapena zinthu zina?
Kuwerenga Baibulo: (4 min.) De 23:1-14 (th phunziro 5)
KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI
“Zimene Mungachite Kuti Muzisangalala Kwambiri mu Utumiki—Muziwafika Pamtima”: (9 min.) Nkhani yokambirana. Onerani vidiyo yakuti Muziwonjezera Luso Lanu Kuti Muzisangalala ndi Ntchito Yophunzitsa—Muziwafika Pamtima.
Nkhani: (5 min.) g 4/15 13—Mutu: Kodi Kupha Nyama N’kulakwa? (th phunziro 14)
MOYO WATHU WACHIKHRISTU
Zofunika Pampingo: (15 min.)
Phunziro la Baibulo la Mpingo: (30 min.) lvs mutu 2 ndime 17-21, Mfundo za M’Baibulo tsa. 27-30, Mawu Akumapeto 7
Mawu Omaliza (3 min.)
Nyimbo Na. 124 ndi Pemphero