August 23-29
DEUTERONOMO 29-30
Nyimbo Na. 3 ndi Pemphero
Mawu Oyamba (1 min.)
CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU
“Kutumikira Yehova Sikovuta Kwambiri”: (10 min.)
Mfundo Zothandiza: (10 min.)
De 29:4—Kodi chitsanzo cha Aisiraeli omwe anali osakhulupirika chimatiphunzitsa chiyani? (it-1 665 ¶3)
Pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno, kodi mwapeza mfundo ziti zokhudza Yehova, utumiki kapena zinthu zina?
Kuwerenga Baibulo: (4 min.) De 29:1-18 (th phunziro 2)
KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI
Ulendo Woyamba: (3 min.) Yambani ndi chitsanzo cha ulendo woyamba. Mugawireni khadi lodziwitsa anthu za jw.org. (th phunziro 1)
Ulendo Wobwereza: (4 min.) Yambani ndi chitsanzo cha ulendo wobwereza. M’pempheni kuti muziphunzira naye Baibulo, ndipo yerekezerani kumuonetsa vidiyo yakuti Kodi Phunziro la Baibulo Limachitika Bwanji? (th phunziro 6)
Phunziro la Baibulo: (5 min.) lvs 226-227 ¶3-5 (th phunziro 13)
MOYO WATHU WACHIKHRISTU
“Kukhala Olimba Mtima Sikovuta Kwambiri”: (15 min.) Nkhani yokambirana. Onerani vidiyo yakuti Musamatsanzire Anthu Amantha, Koma Olimba Mtima.
Phunziro la Baibulo la Mpingo: (30 min.) lvs mutu 3 ndime 16-21, Mfundo za M’Baibulo tsa. 41-44, Mawu Akumapeto 8
Mawu Omaliza (3 min.)
Nyimbo Na. 105 ndi Pemphero