Pitani ku nkhani yake # link, for screen reader ##

Pitani ku mitu ya nkhani

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

Kutumikira Yehova Sikovuta Kwambiri

Kutumikira Yehova Sikovuta Kwambiri

Tikhoza kukwanitsa kuphunzira komanso kutsatira malamulo a Mulungu (De 30:​11-​14; w09 11/1 31 ¶2)

Yehova watipatsa ufulu wosankha (De 30:15; w09 11/1 31 ¶1)

Yehova amafuna kuti tisankhe moyo (De 30:19; w09 11/1 31 ¶4)

Kutumikira Yehova sikungamativute kwambiri ngati titamamudalira kuti azititsogolera komanso kutipatsa mphamvu.