August 30–September 5
DEUTERONOMO 31-32
Nyimbo Na. 78 ndi Pemphero
Mawu Oyamba (1 min.)
CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU
“Zimene Tingaphunzire pa Mafanizo a mu Nyimbo Youziridwa”: (10 min.)
Mfundo Zothandiza: (10 min.)
De 31:12—Kodi makolo Achikhristu angagwiritse ntchito bwanji mfundo ya mulembali? (w04 9/15 27 ¶11)
Pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno, kodi mwapeza mfundo ziti zokhudza Yehova, utumiki kapena zinthu zina?
Kuwerenga Baibulo: (4 min.) De 32:36-52 (th phunziro 2)
KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI
Ulendo Woyamba: (3 min.) Yambani ndi chitsanzo cha ulendo woyamba. Sonyezani mmene mungayankhire munthu amene wanena zinthu zina zomwe anthu amakonda kunena ngati sakufuna kuti tikambirane nawo. (th phunziro 3)
Ulendo Wobwereza: (4 min.) Yambani ndi chitsanzo cha ulendo wobwereza. Sinthani ulaliki wanu kuti ugwirizane ndi nkhani imene mwininyumba watchula, ndipo werengani lemba logwirizana ndi nkhaniyo. (th phunziro 12)
Nkhani: (5 min.) w07 5/15 15-16—Mutu: Ana Anu Amaona Zimene Mumachita (th phunziro 16)
MOYO WATHU WACHIKHRISTU
Anthu Amene Akutsogolera Amatipatsa Chitsanzo Chabwino: (15 min.) Nkhani yokambirana. Onerani vidiyo yakuti ‘Muzikumbukira Amene Akutsogolera’ (Ahe 13:7). Kenako funsani omvera kuti: Kodi tikuphunzira chiyani pa chitsanzo cha M’bale T. J. Sullivan? M’bale George Gangas? M’bale Karl Klein? M’bale Daniel Sydlik?
Phunziro la Baibulo la Mpingo: (30 min.) lvs mutu 4 ndime 1-11, bokosi lakuti Muzimvera Malangizo, Mawu Akumapeto 9-12
Mawu Omaliza (3 min.)
Nyimbo Na. 21 ndi Pemphero