Pitani ku nkhani yake # link, for screen reader ##

Pitani ku mitu ya nkhani

Mose akuphunzitsa anthu a Mulungu nyimbo yolemekeza Yehova

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

Zimene Tingaphunzire pa Mafanizo a mu Nyimbo Youziridwa

Zimene Tingaphunzire pa Mafanizo a mu Nyimbo Youziridwa

Zimene timaphunzitsa anthu zili ngati mame (De 32:​2, 3; w20.06 10 ¶8-9; onani chithunzi chapachikuto)

Yehova ndi Thanthwe (De 32:4; w09 5/1 14 ¶4)

Yehova amateteza anthu ake ngati mmene chiwombankhanga chimatetezera ana ake (De 32:11, 12; w01 10/1 9 ¶7)

Kodi mungapeze kuti mafanizo abwino omwe mungagwiritse ntchito mukamaphunzitsa anthu?