CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU
Kodi Chilamulo Chinkasonyeza Bwanji Kuti Yehova Amaganizira Akazi?
Mwamuna sankayenera kusiya mkazi wake n’kupita ku nkhondo m’chaka choyamba cha ukwati wawo (De 24:5; it-2 1196 ¶4)
Akazi amasiye ankapatsidwa zinthu zofunika pamoyo (De 24:19-21; it-1 963 ¶2)
Akazi amasiye omwe analibe ana ankapatsidwa mwayi wokhala ndi ana (De 25:5, 6; w11 3/1 23)
DZIFUNSENI KUTI, ‘Kodi ndingasonyeze bwanji kuti ndimaganizira komanso kulemekeza akazi m’banja langa komanso mumpingo?’