July 19-25
DEUTERONOMO 16-18
Nyimbo Na. 115 ndi Pemphero
Mawu Oyamba (1 min.)
CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU
“Mfundo Zothandiza Kuweruza Milandu Mwachilungamo”: (10 min.)
Mfundo Zothandiza: (10 min.)
De 17:7—N’chifukwa chiyani Chilamulo chinkanena kuti anthu omwe anapereka umboni woti munthu wachita tchimo ndi amene ankayenera kukhala oyamba kumuponya miyala wolakwayo? (it-1 787)
Pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno, kodi mwapeza mfundo ziti zokhudza Yehova, utumiki kapena zinthu zina?
Kuwerenga Baibulo: (4 min.) De 16:9-22 (th phunziro 5)
KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI
Ulendo Woyamba: (3 min.) Yambani ndi chitsanzo cha ulendo woyamba. Gawirani magazini yomwe ili ndi nkhani imene mwininyumba anatchula. (th phunziro 3)
Ulendo Wobwereza: (4 min.) Yambani ndi chitsanzo cha ulendo wobwereza. Gawirani chimodzi mwa Zinthu Zophunzitsira. (th phunziro 4)
Nkhani: (5 min.) it-1 519 ¶4—Mutu: Kodi Mumpingo Wachikhristu Muli Oweruza Milandu? (th phunziro 18)
MOYO WATHU WACHIKHRISTU
Kodi Mungatumikire Monga Mpainiya Wokhazikika?: (10 min.) Nkhani yokambirana yokambidwa ndi woyang’anira utumiki yochokera munkhani zakuti “Kodi Mungachite Upainiya kwa Chaka Chimodzi?” ndi “Ndandanda ya Upainiya Wokhazikika,” zopezeka mu Ndandanda ya Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu ya July 2016. Onerani ndi kukambirana mfundo za muvidiyo yakuti Yehova Amatithandiza Tikamachita Utumiki Wathu.
Zofunika Pampingo: (5 min.)
Phunziro la Baibulo la Mpingo: (30 min.) lvs mutu 2 ndime 1-7, Mawu Akumapeto 5
Mawu Omaliza (3 min.)
Nyimbo Na. 34 ndi Pemphero