July 5-11
DEUTERONOMO 11-12
Nyimbo Na. 40 ndi Pemphero
Mawu Oyamba (1 min.)
CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU
“Kodi Yehova Amafuna Kuti Tizimulambira Bwanji?”: (10 min.)
Mfundo Zothandiza: (10 min.)
De 11:29—Kodi n’kutheka kuti lembali linakwaniritsidwa bwanji? (it-1 925-926)
Pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno, kodi mwapeza mfundo ziti zokhudza Yehova, utumiki kapena zinthu zina?
Kuwerenga Baibulo: (4 min.) De 11:1-12 (th phunziro 2)
KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI
“Zimene Mungachite Kuti Muzisangalala Kwambiri mu Utumiki—Muzisonyeza Kuti Mumawaganizira”: (8 min.) Nkhani yokambirana. Onerani vidiyo yakuti Muziwonjezera Luso Lanu Kuti Muzisangalala ndi Ntchito Yophunzitsa—Muzisonyeza Kuti Mumawaganizira.
Vidiyo ya Ulendo Woyamba: (4 min.) Nkhani yokambirana. Onerani vidiyo yakuti Ulendo Woyamba: Kuvutika—Yak 1:13. Muziimitsa vidiyoyi nthawi iliyonse imene pali chizindikiro chosonyeza kuti muime n’kufunsa omvera mafunso omwe ali muvidiyoyi.
Ulendo Woyamba: (2 min.) Gwiritsani ntchito chitsanzo cha ulendo woyamba. (th phunziro 1)
MOYO WATHU WACHIKHRISTU
Zofunika Pampingo: (15 min.)
Phunziro la Baibulo la Mpingo: (30 min.) lvs mutu 1 ndime 7-12, Mawu Akumapeto 2, 3
Mawu Omaliza (3 min.)
Nyimbo Na. 108 ndi Pemphero