August 1-7
1 MAFUMU 1-2
Nyimbo Na. 98 ndi Pemphero
Mawu Oyamba (1 min.)
CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU
“Kodi Mumaphunzirapo Kanthu Mukalakwitsa Zinazake?”: (10 min.)
Mfundo Zothandiza: (10 min.)
1Mf 2:37, 41-46—Kodi tingaphunzire chiyani pa zimene Simeyi analakwitsa? (w05 7/1 30 ¶2)
Pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno, kodi mwapeza mfundo ziti zokhudza Yehova, utumiki kapena zinthu zina?
Kuwerenga Baibulo: (4 min.) 1Mf 1:28-40 (th phunziro 2)
KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI
Ulendo Woyamba: (3 min.) Gwiritsani ntchito nkhani imene ili mu chitsanzo cha ulendo woyamba. Mugawireni khadi lodziwitsa anthu za jw.org. (th phunziro 11)
Ulendo Wobwereza: (4 min.) Yambani ndi nkhani imene ili mu chitsanzo cha ulendo wobwereza. Kenako yerekezerani kumuonetsa vidiyo yakuti Kodi pa Nyumba ya Ufumu Pamachitika Zotani? ndipo muitanireni ku misonkhano yathu. (th phunziro 20)
Nkhani: (5 min.) km 1/15 2 ¶1-3—Mutu: Muziphunzira Kuchokera kwa Anthu Amene Amalalikira Mogwira Mtima. (th phunziro 13)
MOYO WATHU WACHIKHRISTU
“Mukhale ndi Zolinga mu Chaka Chautumiki Chikubwerachi—Funsirani Sukulu ya Akhristu Olalikira za Ufumu”: (7 min.) Nkhani yokambirana. Onerani vidiyo yakuti Lowani pa Khomo la Utumiki Mwachikhulupiriro—Funsirani Sukulu ya Akhristu Olalikira za Ufumu.
“Mukhale ndi Zolinga mu Chaka Chautumiki Chikubwerachi—Thandizani pa Ntchito Yazomangamanga”: (8 min.) Nkhani yokambirana. Onerani vidiyo yakuti Lowani pa Khomo la Utumiki Mwachikhulupiriro—Thandizani pa Ntchito Yazomangamanga.
Phunziro la Baibulo la Mpingo: (30 min.) lff phunziro 14
Mawu Omaliza (3 min.)
Nyimbo Na. 24 ndi Pemphero